Lyrics

Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Mayo ndakulakwiranji iwe? Mayo bwenzi lokondeka iwe Mayo mtima ukuwawa bwanji iwe? Mayo ndiyankhe tsopanoli iwe Mtundu wanga, mtundu wanga iwe Ndakulakwitra chani iwe? Kuti mpakana undiphe iwe Panalibe chilango china kodi iwe? Chomwe ukanandipatsa ine Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Kodi ndine woyamba iwe? Kuti ndikulakwire iwe Sindinayembekezele iwe Kuti mpaka ungandiphe iwe Ndisanakaweluzidwe ine Mayo wandipha ngati njoka ine Mayo kodi umapemphera iwe? Mayo kuyesa kufuula ine Mayo osamva chisoni iwe Pomwe umkandigwira iwe Sindinafune kuthawa ine Poti ndinali kudziwa ine Kuti ndiwe mtundu wanga iwe Tikakambirana zizatha iwe Mayo kundimenya njira yonse iwe Mayo pomangidwa mikono ine Mayo tunthu wanga ndisiye iwe Mayo ndafa imfa ya njoka ine .Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah .Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out