Lyrics

Yeah yeah yeah yeah ooh Aaah ooh oh ooh! Uh yeah yeah Uh yeah yeah Silver, Njuchi Kunali chimdima Ndidadabwa kadzanja kakundikodola Nditawonetsetsa anali mkazi wokongola Timawu tamtatamya mkudzati tandilondola I still feel 'dem Ndili munjira adayamba kundiuza nkhani Eli uli ndi luso labho chamkatikati Tikudziwa wakumana ndi zokhoma But we don't know ngati unaganizirako za Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe Illuminat, kuti ma babe amufile Nyimbo zake zimveke Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe Illuminat illumina-illumina illuminat Me don't know now Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat She started saying things like she was reading my mind Ukango joiner wapeza ulemelero Upeza zonse zomwe umafunitsitsa zija Ugwira chimkazi chomwe umafuna chija Zomwe tikufuna kwa iweyo ndi zochepa Ungozimitsa a Chizmo ndi a Veda Komaso tifuna a Chifuniro aja Nditavomela kunatseguka chikhomo Kunali chiphwando Zomwe ndimkaona zinali zachilendo Kudabwana Dada Chai-Khun ali pampando Ndekuti nzika zinalandila kale udindo (Njuchi) Mr Kauden anabweletsa mbale Ndinanyamula mpeni oti ineyo ndibayile Ndinalira nditawona abale anga Akumenya pemphero lawo la madzulo Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe Illuminat, kuti ma babe amufile Nyimbo zake zimveke Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe Illuminat illumina-illumina illuminat Me don't know now Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat Kunali chimdima Ndidadabwa kadzanja kakundikodola Nditaonetsetsa anali mkazi wokongola Timawu tamtatamya mkudzati tandilondola I still feel 'dem Ndili munjira adayamba kundiuza nkhani Eli uli ndi luso labho chamkatikati Tikudziwa wakumana ndi zokhoma But we don't know ngati unaganizirako za Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe Illuminat, kuti ma babe amufile Nyimbo zake zimveke Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe Illuminat illumina-illumina illuminat (yeah yeah yeah) Me don't know now (Eli) Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat Eyo Zuka Me don't know
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out