Lyrics

(Sonye on the beat) Eh ooh ooh ooh! Ndamva kulira zinganga Nthungululu ndi ng'oma pokopoko Ndawonera anamwali kutchena Anyamata wonunkhira perfume Ndamva dj khutchukhutchu Anyamata, asungwana okonda dance Akuponya ndalama ponse ponse Mabotolo a champagne bu-bu-bu Thamangani abale mudzaone Anzathu ndi ukwati woyera Akuchimuna kukonda castel Akuchikazi nawo ku challenger Mkazamupeza nane wachikondi Kulikonse nzayenda naye Mkazamupeza nane wachikondi Kulikonse nzayenda naye Kuyenda ngati ngumbi Kuyenda ngati ngumbi, (ooh) Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe, (oh nyada) Kuyenda ngati ngumbi Zothothola mapiko Kuyenda ngati ngumbi Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe Uyende ngati ngumbi Zothothola mapiko Bayibulo limatiwuza Sibwino anthu wokondana Kumakhala motalikana Usapeleke mwayi kwa satana Muphunzire kudyela pamodzi Kupita kumunda limodzi Ku chikwati kupita limodzi Kukasambaso limodzi Kuyenda ngati ngumbi Kuyenda ngati ngumbi, (kuyenda ngati ngumbi) Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe, (oh nyada) Kuyenda ngati ngumbi Zothothola mapiko Kuyenda ngati ngumbi Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe Uyende ngati ngumbi Zothothola mapiko Oh huu! Oh ooh Pang'ono, pang'ono Eh Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono Uh huh, uh huh, uh huh Uh huh, uh huh, uh huh Kuyenda, kuyenda Kuyenda ngati, kuyenda ngati Kuyenda ngati nkhunda aah Kuyenda ngati, kuyenda ngati Kuyenda ngati nkhunda aah Kuyenda ngati ngumbi Kuyenda ngati ngumbi, (kuyenda ngati ngumbi) Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe Kuyenda ngati ngumbi Zothothola mapiko Kuyenda ngati ngumbi Kulikonse limodzi Kuyenda ngati nkhunda Moyo wathu wonse Chikondi nchosowa Ukachipeza iwe Uyende ngati ngumbi Zothothola mapiko Oh huu! Ooh ooh Pang'ono, pang'ono Eh pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono Pang'ono, pang'ono, pang'ono (Pang'ono)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out